notícias musicais

top 13 artistas

top 13 musicas

Confira a Letra Tropical Winter

The National Parcs

Tropical Winter

VERSE I

Podzuka khungu lauma ndipo lang'aluka
(On waking up my skin is dry and cracked)

Lero ndikatuluka ndikhale okonzeka
(Today when I leave I should be ready)

Khasu liri pamtengo kudikila kupita kumunda
(The hoe is waiting by the tree to go to the garden)

Ine ndi anzanga tikuti lero kwatentha
(My friends and I are saying today is hot)

Tasosa ndipo tadzala ngati masiku onse
(We have weeded and planted as always)

Ndamanga chisoti ndi luzi kuti chisabvuke
(I have tied my hat with rope so that it doesn't come off)

Dzuwa ndi mfumu litiuza kuti tipume
(The sun is king and it will tell us that we should rest)

Ndiye tiyenela kulimvela kuti lisatioche
(And so we should listen so that it doesn't burn us)

VERSE II

Mzanga waona mitambo yodabwitsa
(My friend has seen strange clouds)

Mitambo yoyela komanso ya mphepo yo zizira
(The clouds are white and the wind is cold)

Ine sindimaganiza kuti ndidzaziona
(I never thought that I would see this)
Thukuta lauma ndipo phulusa loyela likugwa
(My sweat is dry and white ash is falling)

Azimai akuti
(The women are saying)

VERSE III

Azibambo akukambilana za mawa
(The men are discussing about tomorrow)

Tracker