notícias musicais

top 13 artistas

top 13 musicas

Confira a Letra Maury

Namadingo

Maury

Namadingo
Kumvetsetsana
Inde tinkamvetsetsana
Ija inali true love

Tinkakondana ah ah ah
Zatsogolo lathu
Zidali mmanja mwake
Mwa Mulungu

Koma yemwe adanena
Palibe chosatha
Sadanane
Zonse zimatha ah ah

Zimawawa palibe chamuyaya ah ah ah ah
Maury adandisiya
Maury adakwatiwa
Ine zidandiwawa koma

(Ululu umatha ah ah ah)
Pakapita nthawi ine
(Mabala achila ah ah ah)
Maury adandisiya komabe

(Ululu umatha ah ah ah)
Moyo goes on
(Mabala achila ah ah ah)
Palibe chamuyaya

Papita nthawi ine
Maury atandisiya
Maury adakwatiwa
Atapita Maury

Nalo dziko lilandikulira
Mtima kupweteka nkumangopirira
(Kupirira)
Pagulu ukumwetulira

Kumbali ukusisima
Ukulira
Maganizo kukumbuka momwe
Chikondi chinkakomera

Simomwe mtima wako nawonso
Umawawira
Kutopa ndi kulira maso ku fiila
Kufuna kudzimangirira ah ah ah

Koma ayi ayi uh huh
Zonse zimatha mchimwene wanga
Palibe chosatha mchemwali wanga
Zimawawa komabe

Ululu umatha ah ah ah
Papita nthawi komabe
Mabala achila ah ah ah
Ine Maury adandisiya

Komabe ululu umatha ah ah ah
Ndipo mabala achila ah ah ah
Maury adandisiya
Maury adakwatiwa

(Palibe chosata ah ah ah)
Ndipo palibe chamuya ah ah ah
Olo ndalama imatha
Iwe kukhala mmaludzi

Maudindo amatha
Iwe kukhala nobody
Olo maludzi amatha
Mutaipedza bandulo

Inu minyama imatha
Iwe kupedza madalitso
Ungo limba mtima
(Moyo ndi choncho moyo oh oh oh)

Tsiku lina udzachira
(Moyo ndi choncho moyo oh oh oh)

Tracker